-
Ezekieli 41:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Pakhoma la kachisiyo, kuyambira pansi mpaka pamwamba pa khomo, anajambulapo mochita kugoba zithunzi za akerubi ndi za mitengo ya kanjedza.
-