Ezekieli 42:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Kenako munthu uja anandipititsa kubwalo lakunja mbali yakumpoto.+ Ndiyeno anandipititsa kunyumba imene inali ndi zipinda zodyera yomwe inali pafupi ndi malo opanda kanthu,+ kumpoto kwa nyumba imene inali kumadzulo.*+
42 Kenako munthu uja anandipititsa kubwalo lakunja mbali yakumpoto.+ Ndiyeno anandipititsa kunyumba imene inali ndi zipinda zodyera yomwe inali pafupi ndi malo opanda kanthu,+ kumpoto kwa nyumba imene inali kumadzulo.*+