-
Ezekieli 42:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Zipinda zodyera zamʼmwamba zinali zocheperapo kusiyana ndi zapakati komanso zapansi chifukwa chakuti makonde anatenga malo ena a zipindazo.
-