Ezekieli 42:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anayeza malowo mbali zonse 4. Malo onsewo anali ndi mpanda+ umene unali mabango 500 mulitali ndi mabango 500 mulifupi mwake.+ Mpandawo unkasiyanitsa malo opatulika ndi malo wamba.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 42:20 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, ptsa. 26-27
20 Anayeza malowo mbali zonse 4. Malo onsewo anali ndi mpanda+ umene unali mabango 500 mulitali ndi mabango 500 mulifupi mwake.+ Mpandawo unkasiyanitsa malo opatulika ndi malo wamba.+