Ezekieli 43:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumeneko ndinaona ulemerero wa Mulungu wa Isiraeli ukubwera kuchokera kumʼmawa+ ndipo mawu ake ankamveka ngati mkokomo wa madzi.+ Dziko lapansi linawala chifukwa cha ulemerero wake.+
2 Kumeneko ndinaona ulemerero wa Mulungu wa Isiraeli ukubwera kuchokera kumʼmawa+ ndipo mawu ake ankamveka ngati mkokomo wa madzi.+ Dziko lapansi linawala chifukwa cha ulemerero wake.+