Ezekieli 43:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno ulemerero wa Yehova unalowa mʼkachisi* kudzera pageti limene linayangʼana kumʼmawa.+