-
Ezekieli 43:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Iye anandiuza kuti:
“Iwe mwana wa munthu, awa ndi malo a mpando wanga wachifumu+ ndiponso poikapo mapazi anga.+ Ndidzakhala pamalo amenewa, pakati pa Aisiraeli mpaka kalekale.+ Nyumba ya Isiraeli ndi mafumu awo sadzaipitsanso dzina langa loyera+ pochita uhule ndi milungu ina komanso ndi mitembo ya mafumu awo.
-