Ezekieli 43:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma iwe mwana wa munthu, ufotokozere nyumba ya Isiraeli za kachisiyu+ kuti achite manyazi chifukwa cha zolakwa zawo,+ ndipo iwo aonetsetse pulani ya kachisiyu* kuti adziwe mmene anamangidwira. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 43:10 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,9/2017, tsa. 2 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 162
10 Koma iwe mwana wa munthu, ufotokozere nyumba ya Isiraeli za kachisiyu+ kuti achite manyazi chifukwa cha zolakwa zawo,+ ndipo iwo aonetsetse pulani ya kachisiyu* kuti adziwe mmene anamangidwira.