Ezekieli 43:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ana a Zadoki, omwe ndi Alevi ansembe,+ amene amayandikira kwa ine nʼkumanditumikira, uwapatse ngʼombe yaingʼono yamphongo kuchokera pagulu la ziweto kuti ikhale nsembe yamachimo,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
19 Ana a Zadoki, omwe ndi Alevi ansembe,+ amene amayandikira kwa ine nʼkumanditumikira, uwapatse ngʼombe yaingʼono yamphongo kuchokera pagulu la ziweto kuti ikhale nsembe yamachimo,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.