20 ‘Utenge magazi akewo pangʼono nʼkuwapaka panyanga 4 za guwa lansembe komanso mʼmakona 4 a chigawo chachitatu cha guwalo. Uwapakenso pakakhoma konse kozungulira chigawo chachitatucho kuti uyeretse guwa lansembelo ku machimo ndiponso kuti uliperekere nsembe yophimba machimo.+