Ezekieli 44:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma mtsogoleri wa anthu azidzakhala mʼkanyumba kapageti kameneka kuti azidzadya chakudya pamaso pa Yehova+ chifukwa iye ndi mtsogoleri. Azidzalowa mmenemo kudzera kukhonde la kanyumbako ndipo azidzatulukiranso komweko.”+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:3 Nsanja ya Olonda,3/1/1999, tsa. 16
3 Koma mtsogoleri wa anthu azidzakhala mʼkanyumba kapageti kameneka kuti azidzadya chakudya pamaso pa Yehova+ chifukwa iye ndi mtsogoleri. Azidzalowa mmenemo kudzera kukhonde la kanyumbako ndipo azidzatulukiranso komweko.”+