-
Ezekieli 44:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Uuze anthu opandukawo, a nyumba ya Isiraeli kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Mwanyanya kuchita zinthu zonyansa, inu a nyumba ya Isiraeli.
-