-
Ezekieli 44:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Mlendo aliyense amene akukhala mu Isiraeli yemwe sanachite mdulidwe wamumtima ndi mdulidwe wa khungu, asalowe mʼmalo anga opatulika.”
-