Ezekieli 44:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Alevi amene anachoka kwa ine nʼkupita kutali+ pa nthawi imene Aisiraeli anachoka kwa ine nʼkuyamba kutsatira mafano awo onyansa* adzakumana ndi zotsatira za zochita zawo zoipa. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:10 Nsanja ya Olonda,3/1/1999, tsa. 9
10 Koma Alevi amene anachoka kwa ine nʼkupita kutali+ pa nthawi imene Aisiraeli anachoka kwa ine nʼkuyamba kutsatira mafano awo onyansa* adzakumana ndi zotsatira za zochita zawo zoipa.