Ezekieli 44:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Asamamete mpala kumutu kwawo+ kapena kusiya tsitsi lakumutu kwawo kuti litalike kwambiri. Iwo azingoyepula tsitsi lakumutu kwawo.
20 Asamamete mpala kumutu kwawo+ kapena kusiya tsitsi lakumutu kwawo kuti litalike kwambiri. Iwo azingoyepula tsitsi lakumutu kwawo.