Ezekieli 44:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iwo aziphunzitsa anthu anga za kusiyana kwa chinthu chopatulika ndi chinthu chomwe si chopatulika. Ndipo aziwaphunzitsanso kusiyana kwa chinthu chodetsedwa ndi chinthu choyera.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:23 Nsanja ya Olonda,8/1/2007, tsa. 113/1/1999, ptsa. 14-159/15/1988, tsa. 27
23 Iwo aziphunzitsa anthu anga za kusiyana kwa chinthu chopatulika ndi chinthu chomwe si chopatulika. Ndipo aziwaphunzitsanso kusiyana kwa chinthu chodetsedwa ndi chinthu choyera.+