Ezekieli 45:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 “‘Mukamagawana dzikoli kuti likhale cholowa chanu,+ mudzatenge malo ena nʼkuwapereka kwa Yehova monga gawo loyera.+ Malowo adzakhale mikono 25,000* mulitali ndi mikono 10,000 mulifupi.+ Malo onsewo* adzakhale gawo loyera. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:1 Nsanja ya Olonda,3/1/1999, ptsa. 10, 17
45 “‘Mukamagawana dzikoli kuti likhale cholowa chanu,+ mudzatenge malo ena nʼkuwapereka kwa Yehova monga gawo loyera.+ Malowo adzakhale mikono 25,000* mulitali ndi mikono 10,000 mulifupi.+ Malo onsewo* adzakhale gawo loyera.