Ezekieli 45:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mkati mwa gawo loyeralo mudzakhale malo ofanana mbali zonse kuti adzakhale malo oyera. Malowa adzakhale mikono 500 mbali zonse*+ ndipo kumbali iliyonse kudzakhale malo odyetserako ziweto okwana mikono 50.+
2 Mkati mwa gawo loyeralo mudzakhale malo ofanana mbali zonse kuti adzakhale malo oyera. Malowa adzakhale mikono 500 mbali zonse*+ ndipo kumbali iliyonse kudzakhale malo odyetserako ziweto okwana mikono 50.+