Ezekieli 45:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kudzakhale malo okwana mikono 25,000 mulitali ndi mikono 10,000 mʼlifupi.+ Malo amenewa adzakhale a Alevi, omwe ndi atumiki apakachisi. Aleviwo adzakhale ndi zipinda 20 zoti azidzadyeramo chakudya.+
5 Kudzakhale malo okwana mikono 25,000 mulitali ndi mikono 10,000 mʼlifupi.+ Malo amenewa adzakhale a Alevi, omwe ndi atumiki apakachisi. Aleviwo adzakhale ndi zipinda 20 zoti azidzadyeramo chakudya.+