Ezekieli 45:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mudzapereke malo okwana mikono 25,000 mulitali (mofanana ndi chopereka chopatulika) ndi mikono 5,000 mulifupi+ kuti adzakhale malo a mzinda. Malo amenewa adzakhale a anthu a nyumba yonse ya Isiraeli.
6 Mudzapereke malo okwana mikono 25,000 mulitali (mofanana ndi chopereka chopatulika) ndi mikono 5,000 mulifupi+ kuti adzakhale malo a mzinda. Malo amenewa adzakhale a anthu a nyumba yonse ya Isiraeli.