-
Ezekieli 45:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Malo a mtsogoleri wa anthu adzakhale kumbali zonse za chopereka chopatulika komanso za malo amene aperekedwa kuti akhale a mzinda. Adzayandikane ndi chopereka chopatulika komanso malo a mzindawo. Malo a mtsogoleriwo adzakhale kumadzulo ndi kumʼmawa. Mulitali mwake kuchokera kumalire akumadzulo kukafika kumalire akumʼmawa adzakhale ofanana ndi kutalika kwa gawo la fuko la Isiraeli limene layandikana nawo.+
-