Ezekieli 45:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Malo amenewa adzakhale cholowa cha mtsogoleriyo mu Isiraeli. Atsogoleri anga sadzazunzanso anthu anga+ ndipo adzagawa dzikoli kwa anthu a nyumba ya Isiraeli mogwirizana ndi mafuko awo.’+
8 Malo amenewa adzakhale cholowa cha mtsogoleriyo mu Isiraeli. Atsogoleri anga sadzazunzanso anthu anga+ ndipo adzagawa dzikoli kwa anthu a nyumba ya Isiraeli mogwirizana ndi mafuko awo.’+