Ezekieli 45:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Sekeli*+ imodzi izikwana magera* 20. Muziphatikiza masekeli 20, masekeli 25 ndi masekeli 15 kuti ukhale muyezo wanu umodzi wa mane.*
12 Sekeli*+ imodzi izikwana magera* 20. Muziphatikiza masekeli 20, masekeli 25 ndi masekeli 15 kuti ukhale muyezo wanu umodzi wa mane.*