-
Ezekieli 45:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Muzipereka zinthu izi kuti chikhale chopereka chanu: Pa tirigu wanu wokwana homeri, muzipereka gawo limodzi mwa magawo 6 a muyezo wa efa. Ndipo pa balere wanu wokwana homeri muzipereka gawo limodzi mwa magawo 6 a muyezo wa efa.
-