Ezekieli 45:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Poyeza mafuta oti muzipereka, muzigwiritsa ntchito mtsuko woyezera. Mtsuko woyezera ndi wokwana gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa kori.* Mitsuko 10 ndi yokwana homeri chifukwa mitsuko 10 imakwana homeri imodzi.
14 Poyeza mafuta oti muzipereka, muzigwiritsa ntchito mtsuko woyezera. Mtsuko woyezera ndi wokwana gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa kori.* Mitsuko 10 ndi yokwana homeri chifukwa mitsuko 10 imakwana homeri imodzi.