-
Ezekieli 45:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Koma mtsogoleri ndi amene adzakhale ndi udindo woyangʼanira nsembe zopsereza zathunthu,+ nsembe yambewu+ ndi nsembe yachakumwa. Iye azidzayangʼanira nsembezo pa nthawi ya zikondwerero,+ pa masiku amene mwezi watsopano waoneka, pa masiku a Sabata+ ndi pa nthawi ya zikondwerero zonse za nyumba ya Isiraeli.+ Mtsogoleriyo ndi amene azidzapereka kwa ansembe nsembe yamachimo, nsembe yambewu, nsembe yopsereza yathunthu ndi nsembe zamgwirizano kuti aphimbe machimo a nyumba ya Isiraeli.’
-