Ezekieli 45:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Mʼmwezi woyamba, pa tsiku loyamba la mweziwo, uzitenga ngʼombe yamphongo yaingʼono yopanda chilema kuchokera pagulu la ziweto, ndipo uziyeretsa kachisi ku machimo.+
18 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Mʼmwezi woyamba, pa tsiku loyamba la mweziwo, uzitenga ngʼombe yamphongo yaingʼono yopanda chilema kuchokera pagulu la ziweto, ndipo uziyeretsa kachisi ku machimo.+