Ezekieli 45:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Wansembe azitenga ena mwa magazi a nsembe yamachimo nʼkuwapaka pafelemu la kachisi,+ mʼmakona 4 a chigawo chachitatu cha guwa lansembe komanso pafelemu la kanyumba kapageti ka bwalo lamkati.
19 Wansembe azitenga ena mwa magazi a nsembe yamachimo nʼkuwapaka pafelemu la kachisi,+ mʼmakona 4 a chigawo chachitatu cha guwa lansembe komanso pafelemu la kanyumba kapageti ka bwalo lamkati.