Ezekieli 45:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Muzichita zimenezi pa tsiku la 7 la mweziwo chifukwa cha munthu aliyense amene wachimwa mwangozi kapena mosadziwa+ ndipo muziyeretsa kachisi ku machimo.+
20 Muzichita zimenezi pa tsiku la 7 la mweziwo chifukwa cha munthu aliyense amene wachimwa mwangozi kapena mosadziwa+ ndipo muziyeretsa kachisi ku machimo.+