Ezekieli 45:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa tsiku limeneli, mtsogoleri azipereka kwa ansembe ngʼombe yaingʼono yamphongo kuti ikhale nsembe yamachimo ake komanso a anthu onse amʼdzikoli.+
22 Pa tsiku limeneli, mtsogoleri azipereka kwa ansembe ngʼombe yaingʼono yamphongo kuti ikhale nsembe yamachimo ake komanso a anthu onse amʼdzikoli.+