24 Popereka ngʼombe iliyonse yaingʼono yamphongo aziperekanso nsembe yambewu yokwana muyezo umodzi wa efa. Popereka nkhosa iliyonse yamphongo aziperekanso nsembe yambewu yokwana muyezo umodzi wa efa. Pa muyezo uliwonse wa efa azipereka mafuta okwana muyezo umodzi wa hini.