-
Ezekieli 46:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Mtsogoleri azilowa kuchokera panja kudzera pakhonde la kanyumba kapagetiko+ ndipo aziima pafupi ndi felemu lagetilo. Ndiyeno ansembe azimuperekera nsembe yopsereza yathunthu ndi nsembe zake zamgwirizano. Mtsogoleriyo azigwada nʼkuwerama pakhomo la kanyumba kapageti kenako nʼkutuluka. Koma getilo lisamatsekedwe mpaka madzulo.
-