5 Popereka nkhosa yamphongo aziperekanso nsembe yambewu yokwana muyezo umodzi wa efa. Popereka ana a nkhosa amphongo aziperekanso nsembe yambewu imene angakwanitse. Pa nsembe iliyonse yambewu yokwana muyezo wa efa azipereka mafuta okwana muyezo wa hini.+