-
Ezekieli 46:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Mukamachita zikondwerero komanso pa nthawi ya zikondwerero zanu, azipereka ngʼombe yaingʼono yamphongo pamodzi ndi nsembe yambewu yokwana muyezo umodzi wa efa. Aziperekanso nkhosa yamphongo pamodzi ndi nsembe yambewu yokwana muyezo umodzi wa efa. Akamapereka ana a nkhosa amphongo aziperekanso nsembe yambewu imene angakwanitse. Pa nsembe iliyonse yambewu yokwana muyezo wa efa azipereka mafuta okwana muyezo wa hini.+
-