-
Ezekieli 46:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Mtsogoleri wa anthu akapereka mphatso kwa mwana wake aliyense wamwamuna monga cholowa chake, mphatsoyo idzakhala chuma cha ana akewo. Chimenecho ndi chuma cha anawo ndipo chidzakhala cholowa chawo.
-