-
Ezekieli 46:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Mtsogoleri wa anthu asamakakamize munthu aliyense kuti achoke pamalo omwe ndi cholowa chake nʼkutenga malowo kuti akhale ake. Ana ake aamuna aziwapatsa cholowa kuchokera pamalo amene ali nawo, kuti pakati pa anthu anga pasapezeke munthu aliyense amene wathamangitsidwa pamalo ake.’”
-