Ezekieli 47:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Asodzi adzaima mʼmbali mwa nyanjayo kuchokera ku Eni-gedi+ mpaka ku Eni-egilaimu, kumene kudzakhale malo oyanikapo makoka. Kudzakhala nsomba zambirimbiri zamitundu yosiyanasiyana ngati nsomba za ku Nyanja Yaikulu.*+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 47:10 Nsanja ya Olonda,3/1/1999, tsa. 21
10 Asodzi adzaima mʼmbali mwa nyanjayo kuchokera ku Eni-gedi+ mpaka ku Eni-egilaimu, kumene kudzakhale malo oyanikapo makoka. Kudzakhala nsomba zambirimbiri zamitundu yosiyanasiyana ngati nsomba za ku Nyanja Yaikulu.*+