Ezekieli 47:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Malire a dzikoli kumbali yakumpoto ndi awa: Akuyambira ku Nyanja Yaikulu kudzera njira ya ku Heteloni+ nʼkumalowera ku Zedadi,+
15 Malire a dzikoli kumbali yakumpoto ndi awa: Akuyambira ku Nyanja Yaikulu kudzera njira ya ku Heteloni+ nʼkumalowera ku Zedadi,+