Ezekieli 47:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ku Hamati,+ ku Berota,+ ku Siburaimu, amene ali pakati pa dera la Damasiko ndi dera la Hamati, mpaka kukafika ku Hazere-hatikoni kufupi ndi malire a Haurani.+
16 ku Hamati,+ ku Berota,+ ku Siburaimu, amene ali pakati pa dera la Damasiko ndi dera la Hamati, mpaka kukafika ku Hazere-hatikoni kufupi ndi malire a Haurani.+