Ezekieli 47:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho malirewo adzayambire kunyanja mpaka ku Hazara-enoni,+ kumene ndi kumalire akumpoto kwa Damasiko komanso kumalire a Hamati.+ Amenewa ndi malire akumpoto.
17 Choncho malirewo adzayambire kunyanja mpaka ku Hazara-enoni,+ kumene ndi kumalire akumpoto kwa Damasiko komanso kumalire a Hamati.+ Amenewa ndi malire akumpoto.