Ezekieli 47:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Malire a mbali yakumʼmawa ali pakati pa Haurani ndi Damasiko, kudutsa mʼmbali mwa mtsinje wa Yorodano pakati pa Giliyadi+ ndi dziko la Isiraeli. Mudzayeze mtunda wochokera kumalirewo kukafika kunyanja yakumʼmawa.* Amenewa ndi malire akumʼmawa.
18 Malire a mbali yakumʼmawa ali pakati pa Haurani ndi Damasiko, kudutsa mʼmbali mwa mtsinje wa Yorodano pakati pa Giliyadi+ ndi dziko la Isiraeli. Mudzayeze mtunda wochokera kumalirewo kukafika kunyanja yakumʼmawa.* Amenewa ndi malire akumʼmawa.