Ezekieli 47:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Malire a mbali yakumʼmwera, adzayambire ku Tamara kukafika kumadzi a Meribati-kadesi,+ kenako akafike kuchigwa cha Iguputo mpaka ku Nyanja Yaikulu.+ Amenewa ndi malire akumʼmwera.
19 Malire a mbali yakumʼmwera, adzayambire ku Tamara kukafika kumadzi a Meribati-kadesi,+ kenako akafike kuchigwa cha Iguputo mpaka ku Nyanja Yaikulu.+ Amenewa ndi malire akumʼmwera.