Ezekieli 48:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Gawo la fuko la Efuraimu lichite malire ndi gawo la fuko la Manase,+ kuyambira kumalire akumʼmawa kukafika kumalire akumadzulo.
5 Gawo la fuko la Efuraimu lichite malire ndi gawo la fuko la Manase,+ kuyambira kumalire akumʼmawa kukafika kumalire akumadzulo.