-
Ezekieli 48:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Mupereke gawo lina kuti likhale chopereka chanu. Gawolo lichite malire ndi gawo la fuko la Yuda kuyambira kumalire akumʼmawa kukafika kumalire akumadzulo ndipo likhale mikono 25,000* mulifupi.+ Mulitali mwake lifanane ndi magawo a mafuko aja kuyambira kumalire akumʼmawa kukafika kumalire akumadzulo. Malo opatulika akhale pakati pa gawo limeneli.
-