-
Ezekieli 48:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Aleviwo asamagulitse, kusinthanitsa kapena kupereka kwa munthu wa fuko lina mbali iliyonse ya malo abwino kwambiriwo, chifukwa malo amenewo ndi opatulika kwa Yehova.
-