Ezekieli 48:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Malo otsala okwana mikono 5,000 mulifupi ndi mikono 25,000 mulitali, akhale malo a mzinda oti munthu aliyense angagwiritse ntchito.+ Malo amenewa akhale oti anthu azimangako nyumba komanso kudyetserako ziweto. Mzinda ukhale pakati pa malowa.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 48:15 Nsanja ya Olonda,8/1/2007, tsa. 113/1/1999, ptsa. 18, 22
15 Malo otsala okwana mikono 5,000 mulifupi ndi mikono 25,000 mulitali, akhale malo a mzinda oti munthu aliyense angagwiritse ntchito.+ Malo amenewa akhale oti anthu azimangako nyumba komanso kudyetserako ziweto. Mzinda ukhale pakati pa malowa.+