-
Ezekieli 48:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Malo onse oti aperekedwe akhale mikono 25,000 mbali zonse 4. Mupereke malo amenewa kuti akhale chopereka chopatulika ndiponso malo a mzinda.
-