Ezekieli 48:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Malire akumʼmwera a dzikolo akhale malire a gawo la fuko la Gadi ndipo achokere ku Tamara+ kukafika kumadzi a Meribati-kadesi,+ kuchigwa cha Iguputo+ mpaka ku Nyanja Yaikulu.*
28 Malire akumʼmwera a dzikolo akhale malire a gawo la fuko la Gadi ndipo achokere ku Tamara+ kukafika kumadzi a Meribati-kadesi,+ kuchigwa cha Iguputo+ mpaka ku Nyanja Yaikulu.*