Danieli 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Mʼchaka chachitatu cha ufumu wa Mfumu Yehoyakimu+ ya Yuda, Mfumu Nebukadinezara ya ku Babulo inabwera ku Yerusalemu ndipo inazungulira mzindawo.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:1 Yeremiya, tsa. 24 Ulosi wa Danieli, ptsa. 18-19, 31-32
1 Mʼchaka chachitatu cha ufumu wa Mfumu Yehoyakimu+ ya Yuda, Mfumu Nebukadinezara ya ku Babulo inabwera ku Yerusalemu ndipo inazungulira mzindawo.+