Danieli 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno mfumu inalamula Asipenazi, mkulu wa nduna zapanyumba ya mfumu kuti abweretse ena mwa Aisiraeli,* kuphatikizapo a mʼbanja lachifumu komanso anthu olemekezeka.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:3 Ulosi wa Danieli, tsa. 33
3 Ndiyeno mfumu inalamula Asipenazi, mkulu wa nduna zapanyumba ya mfumu kuti abweretse ena mwa Aisiraeli,* kuphatikizapo a mʼbanja lachifumu komanso anthu olemekezeka.+